Eksodo 16:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndamva madandaulo a ana a Israyeli; lankhula nao ndi kuti, Madzulo mudzadya nyama, ndi m'mawa mudzakhuta mkate; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Eksodo 16

Eksodo 16:9-17