Eksodo 15:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nyimbo yolemekeza Mulungu, Pamenepo Mose ndi ana a Israyeli anayimbira Yehova nyimbo iyi, nanena, ndi kuti,Ndidzayimbira Yehova pakuti wapambanatu;Kavalo ndi wokwera wace anawaponya m'nyanja.

Eksodo 15

Eksodo 15:1-8