Eksodo 14:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anauza mfumu ya Aigupto kuti anthu adathawa; ndi mtima wa Farao ndi wa anyamata ace inasandulikira anthuwo, ndipo anati, Ici nciani tacita, kuti talola Israyeli amuke osatigwiriranso nchito?

Eksodo 14

Eksodo 14:1-11