Eksodo 14:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anatambasulira dzanja lace kunyanja, ndi nyanja inabwerera m'mayendedwe ace mbanda kuca; ndipo Aaigupto pothawa anakomana nayo; ndipo Yehova anakutumula Aaigupto m'kati mwa nyanja.

Eksodo 14

Eksodo 14:21-31