Eksodo 14:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lankhula ndi anthu a Israyeli kuti abwerere m'mbuyo nagone patsogolo pa Pihahiroti, pakati pa Migidoli ndi nyanja yamcere, patsogolo pa Baala-Zefoni; pandunji pace mugone panyanja.

Eksodo 14

Eksodo 14:1-11