Eksodo 13:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Ndipo anacokera ku Sukoti, nagona ku Etamu, pa malekezero a cipululu.

21. Ndipo Yehova anawatsogolera usana ndi mtambo njo kuwatsogolera m'njira; ndi usiku ndi moto njo, wakuwawalitsira; kuti ayende usana ndi usiku;

22. sanacotsa mtambo usana, kapena mtambo wamoto usiku, pamaso pa anthu.

Eksodo 13