Eksodo 13:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Mulungu anawazungulitsa anthuwo, ku njira ya kucipululu ya Nyanja Yofiira; ndipo ana a Israyeli anakwera kucokera m'dziko la Aigupto okonzeka.

Eksodo 13

Eksodo 13:17-19