Eksodo 13:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma woyamba yense wa buru uzimuombola ndi mwana wa nkhosa; ndipo ukapanda kumuombola uzimthyola khosi; koma oyamba onse a munthu mwa ana ako uziwaombola.

Eksodo 13

Eksodo 13:9-19