Eksodo 12:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma akakhala nanu mlendo, nakonzera Yehova Paskha, adulidwe amuna ace onse, ndipo pamenepo asendere kuucita; nakhale ngati wobadwa m'dziko; koma wosadulidwa ali yense asadyeko.

Eksodo 12

Eksodo 12:47-51