Eksodo 12:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Banja likaperewera mwana wa nkhosa, munthu ndi mnzace ali pafupi pa nyumba yace atenge monga mwa kufikira kwa anthu ao; muziwerengera mwana wa nkhosa monga mwa kudya kwao.

Eksodo 12

Eksodo 12:1-7