Eksodo 12:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaoca timitanda topanda cotupitsa ta mtanda umene anabwera nao ku Aigupto, popeza sadaikamo cotupitsa; pakuti adawapitikitsa ku Aigupto, ndipo sanathe kucedwa, kapena kudzikonzeratu kamba.

Eksodo 12

Eksodo 12:35-40