Eksodo 12:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anayenda ulendo wakucokera ku Ramese kufikira ku Sukoti, zikwi mazana asanu ndi limodzi oyenda okha, ndiwo amuna, osawerenga ana.

Eksodo 12

Eksodo 12:29-42