Eksodo 11:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ana onse oyamba a m'dziko la Aigupto adzafa, kuyambira mwana woyamba wa Farao wokhala pa mpando wacifumu wace, kufikira mwana woyamba wa mdzakazi wokhala pa miyala yopera; ndi ana onse oyamba a zoweta.

Eksodo 11

Eksodo 11:1-10