Eksodo 11:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ndi Aroni anacita zozizwa izi zonse pamaso pa Farao; koma Yehova analimbitsa mtima wace wa Farao, ndipo sanalola ana a Israyeli aturuke m'dziko lace.

Eksodo 11

Eksodo 11:1-10