Eksodo 10:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anyamata ace a Farao ananena naye, Ameneyo amaticitira msampha kufikira liti? Lolani anthuwo amuke, akatumikire Yehova Mulungu wao. Kodi simunayambe kudziwa kuti Aigupto laonongeka?

Eksodo 10

Eksodo 10:4-9