Eksodo 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao; pakuti ndaumitsa mtima wace, ndi mtima wa anyamata ace, kuti ndiike zizindikilo zanga izi pakati pao;

Eksodo 10

Eksodo 10:1-10