Eksodo 1:21-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Ndipo kunatero kuti, popeza anamwino anaopa Mulungu, iye anawamangitsira mabanja.

22. Ndipo Farao analamulira anthu ace onse, ndi kuti, Ana amuna onse akabadwa aponyeni m'nyanja, koma ana akazi onse alekeni amovo.

Eksodo 1