Eksodo 1:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92) NDIPO maina a ana a Israyeli, amene analowa m'Aigupto ndi Yakobo ndi awa, analowa munthu ndi banja lace: Rubeni