Deuteronomo 9:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kumbukilani, musamaiwala, kuti munakwiyitsa Yehova Mulungu wanu m'cipululu; kuyambira tsikuli munaturuka m'dziko la Aigupto, kufikira munalowa m'malo muno munapiktsana ndi Yehova.

Deuteronomo 9

Deuteronomo 9:1-12