Deuteronomo 9:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iwo ndiwo anthu anu ndi colowa canu, amene mudaturutsa ndi mphamvu yanu yaikuru ndi dzanja lanu lotambasuka.

Deuteronomo 9

Deuteronomo 9:20-29