Deuteronomo 9:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinapemphera kwa Yehova ndi kuti, Yehova Mulungu, musaononga anthu anu ndi colowa canu, amene mudawaombola mwa ukulu wanu, amene munawaturutsa m'Aigupto ndi dzanja lamphamvu,

Deuteronomo 9

Deuteronomo 9:24-29