Deuteronomo 9:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa ine, Uka, fulumira kutsika kuno popeza anthu ako unawaturutsa m'Aigupto wa anadziipsa; anapatuka msanga m'njira ndinawalamulirayi; anadzipangira fano loyenga.

Deuteronomo 9

Deuteronomo 9:3-15