Deuteronomo 8:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Muzisamalira kucita malamulo onse amene ndikuuzani lero lino, kuti mukhale ndi moyo, ndi kucuruka, ndi kulowa, ndi kulandira dziko limene Yehova analumbirira makolo anu.

Deuteronomo 8

Deuteronomo 8:1-11