Deuteronomo 7:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova Mulungu wanu adzawapereka pamaso panu, nadzawapitikitsa ndi kupitikitsa kwakukuru, kufikira ataonongeka.

Deuteronomo 7

Deuteronomo 7:18-26