Deuteronomo 6:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo muziwaphunzitsa mwacangu kwa ana anu, ndi kuwalankhula awa pokhala pansi m'nyumba zanu, ndi poyenda inu panjira, ndi pogona inu pansi, ndi pouka inu.

Deuteronomo 6

Deuteronomo 6:5-14