Deuteronomo 6:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muzicita zolunjika ndi zokoma pamaso pa Yehova; kuti cikukomereni, ndi kuti mulowe kukalandira dziko lokomali Yehova analumbirira makolo anu,

Deuteronomo 6

Deuteronomo 6:15-25