Deuteronomo 6:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti Yehova Mulungu wanu ali pakati panu, ndiye Mulungu wansanje; kuti ungapse mtima wa Yehova Mulungu wanu, ndi kukuonongani, kukucotsani pankhope pa dziko lapansi.

Deuteronomo 6

Deuteronomo 6:11-16