Deuteronomo 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzakhala, Yehova Mulungu wanu atakulowetsani m'dziko limene analumbirira makolo anu, Abrahamu, Isake, ndi Yakobo, kuti adzakupatsani ili; midzi yaikuru ndi yokoma, imene simunaimanga;

Deuteronomo 6

Deuteronomo 6:1-15