Deuteronomo 5:5-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. (ndinalinkufma pakati pa Yehova ndi inu muja, kukulalikirani mau a Yehova; popeza munacita mantha cifukwa ca moto, osakwera m'phirimo) ndi kuti:

6. Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakuturutsa m'dziko la Aigupto, m'nyumba ya akapolo.

7. Usakhale nayo milungu yina koma Ine ndekha.

Deuteronomo 5