Deuteronomo 5:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iwe, uime kuno ndi Ine, ndinene ndi iwe malamulo onse, ndi malemba, ndi maweruzo, amene uziwaphunzitsa, kuti awacite m'dziko limene ndiwapatsa likhale lao lao.

Deuteronomo 5

Deuteronomo 5:22-33