Deuteronomo 4:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ndinakuphunzitsani malemba ndi maweruzo, monga Yehova Mulungu wanga anandiuza ine, kuti muzicita cotero pakati pa dziko limene mumkako kulilandira likhale lanu Lanu.

Deuteronomo 4

Deuteronomo 4:1-10