Deuteronomo 4:48-49 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

48. kuyambira ku Aroeri, ndiwo m'mphepete mwa mtsinje wa Arinoni, kufikira phiri la Sioni (ndilo Herimoni),

49. ndi cidikha conse tsidya lija la Yordana kum'mawa, kufikira nyanja ya kucidikha, pa tsinde lace la Pisiga.

Deuteronomo 4