Deuteronomo 4:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti athawireko wakupha munthu, osamupha mnansi wace dala, osamkwiyira ndi kale lonse; ndi kuti, akathawira ku umodzi wa midzi iyi, akhale ndi moyo:

Deuteronomo 4

Deuteronomo 4:34-49