Deuteronomo 4:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mukafuna Yehova Mulungu wanu kumeneko, mudzampeza, ngati mumfunafuna ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse.

Deuteronomo 4

Deuteronomo 4:25-30