Deuteronomo 4:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anandilamulira muja ndikuphunzitseni malemba ndi maweruzo, kuti mukawacite m'dziko limene muolokerako kulilandira likhale lanu lanu.

Deuteronomo 4

Deuteronomo 4:12-16