Deuteronomo 33:6-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Rubeni akhale ndi moyo, asafe,Koma amuna ace akhale owerengeka.

7. Za Yuda ndi izi; ndipo anati,Imvani, Yehova, mau a Yuda,Ndipo mumfikitse kwa anthu ace;Manja ace amfikire;Ndipo mukhale inu thandizo lace pa iwo akumuukira.

8. Ndipo za Levi anati,Tumimu ndi Urimu wanu zikhala ndi wokondedwa wanu,Amene mudamuyesa m'Masa,Amene mudalimbana naye ku madzi a Meriba;

Deuteronomo 33