Deuteronomo 33:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi zinthu zofunikatu za dziko lapansi, ndi kudzala kwace,Ndi cibvomerezo ca iye anakhala m'citsambayo;Mdalitso ufike pa mutu wa Yosefe,Ndi pakati pa mutu wace wa iye wokhala padera ndi abale ace.

Deuteronomo 33

Deuteronomo 33:14-18