Deuteronomo 32:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mafuta a mkaka wang'ombe, ndi mkaka wankhosa,Ndi mafuta a ana a nkhosa,Ndi nkhosa zamphongo za mtundu wa ku Basana, ndi atonde,Ndi imso zonenepa zatirigu;Ndipo munamwa vinyo, mwazi wamphesa,

Deuteronomo 32

Deuteronomo 32:5-19