Deuteronomo 31:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndidziwa kuti nditamwalira ine mudzadziipsa ndithu, ndi kupatuka m'njira imene ndinakuuzani; ndipo cidzakugwerani coipa masiku otsiriza; popeza mudzacita coipa pamaso pa Yehova, kuutsa mkwiyo wace ndi nchito za manja anu.

Deuteronomo 31

Deuteronomo 31:27-30