Deuteronomo 31:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndidziwa kupikisana kwanu, ndi kupulukira kwanu; taonani, pokhala ndikali ndi moyo pamodzi ndi inu lero, mwapikisana ndi Yehova: koposa kotani nanga nditamwalira ine!

Deuteronomo 31

Deuteronomo 31:22-30