Deuteronomo 31:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anauza Yoswa mwana wa Nuni, nati, Khala wamphamvu, nulimbe mtima; pakuti udzalowa nao ana a Israyeli m'dziko limene ndinawalumbirira: ndipo Ine ndidzakhala ndi iwe.

Deuteronomo 31

Deuteronomo 31:13-29