Deuteronomo 31:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Taona, udzagona tulo ndi makolo ako; ndi anthu awa adzauka, oadzatsata ndi cigololo milungu yacilendo ya dziko limene analowa pakati pace, nadzanditava Ine, ndi kutyola cipangano canga ndinapangana naoco.

Deuteronomo 31

Deuteronomo 31:10-20