Deuteronomo 31:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kuti ana ao osadziwa amve, oaphunzire kuopa Yehova Mulungu wanu, masiku onse akukhala ndi moyo inu kudziko kumene muolokera Yordano kulilandira likhale lanu lanu.

Deuteronomo 31

Deuteronomo 31:12-20