Deuteronomo 3:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yairi mwana wa Manase analanda dziko lonse la Arigobi, kufikira malire a Agesuri ndi Amaakati; nalicha dzina lace, Basana Haroti Yairi, kufikira lero lino.)

Deuteronomo 3

Deuteronomo 3:6-15