Deuteronomo 28:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova adzakucurukitsirani zokoma, m'zipatso za thupi lanu, ndi m'zipatso za zoweta zanu, ndi m'zipatso za nthaka yanu, m'dziko limene Yehova analumbirira makolo anu kuti adzakupatsani ilo,

Deuteronomo 28

Deuteronomo 28:5-15