Deuteronomo 28:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzali, mukadzamvera mau a Yehova Mulungu wanu mwacangu, ndi kusamalira kucita malamulo ace onse amene ndikuuzani lero, kuti Yehova Mulungu wanu adzakukulitsani koposa amitundu onse a pa dziko lapansi;

Deuteronomo 28

Deuteronomo 28:1-6