Deuteronomo 27:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose, ndi ansembe Alevi ananena ndi Israyeli wonse, ndi kuti, Khalani cete, imvanitu, Israyeli; lero lino mwasanduka mtundu wa anthu wa Yehova Mulungu wanu.

Deuteronomo 27

Deuteronomo 27:1-17