Deuteronomo 27:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo mulemberepo mau onse a cilamulo ici, mutaoloka; kuti mulowe m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani, dziko moyenda mkaka ndi uci ngati madzi, monga Yehova Mulungu wa makolo anu ananena ndi inu.

Deuteronomo 27

Deuteronomo 27:1-5