Deuteronomo 27:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wotembereredwa munthu wakupanga fano losema kapena loyenga, lonyansidwa nalo Yehova, nchito ya manja a mmisiri, ndi kuliika m'malo a m'tseri. Ndipo anthu onse: ayankhe ndi kuti, Amen.

Deuteronomo 27

Deuteronomo 27:13-25