Deuteronomo 26:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mufike kwa wansembe wakukhala m'masiku awa, ndi kunena naye, Ndibvomereza lero lino kwa Yehova Mulungu wako, kuti ndalowa m'dziko limene Yehova analumbirira makolo athu, kuti adzatipatsa ili.

Deuteronomo 26

Deuteronomo 26:1-9